Kukwera Kumwamba by Talumba Chirwa
I will not give up
There is no expectation that was thrown in my favour to which I will not live up
So let me give God big ups
For helping me when life was rough and I was going through some back hiccups
When your eyes have blurred and your future is bleak
Your dreams defer and the strength you try to cook up is weak
When you don’t even know why you are here
Constant fear, wishing these problems would simply disappear
But I am the voice of the voiceless, so let me speak
I am only human I get hungry, so let me eat
I am only human I am not perfect, so let me be
And if you think that I am blind then please help me see
Zaka zapita zingapo, ndaphunzira zambiri
Miyendo iwiri ithamanga kupotsa chipiriri
Kuthamanga sikufika
Kuthokoza sikoyipa, kuzichepetsa mtima sikutsika
Verse 2
Ndikukwera pamwamba, ndikukhala pamwamba
Ndikubwera ku mbamba ndi ku yenda pa Nyanja
Ana amasikuano ena osavera pa banja
Kudulira koma nsewuwo ukuthera kumanda
Zomvesa chisoni, kuyambira ku Chilomoni
Msungwana koma aliyense wagwirako ngati moni
Nyamata koma aliyense wagwirako ngati foni
Kuyambira achina Chifundo mpakana achina Joni
So what do we do,
Don’t be obsessed with others
Love your Lord, God, Mom, Dad, Sister and Brothers
Love your own soul, grow more showing your colours
Love is so sore, when its raw without any covers
Njala nchilombo, ulesi ndi imfa
Ambiri anyimba, khala tchelu mfana nawenso imva
Pawiri pawiri si pangwirika
Trying to grab two different things at once will leave you with neither
Hook
Pachigaleta chamoto ndikukwera kumwamba
Moyo wanga wonse kukana kupanga zawamba
Pachigaleta chamoto ndikukwera kumwamba
Ndikukwera kumwamba ndi kukhala pamwamba
Thank you for supporting this blog. Follow Talumba Chirwa on Twitter @Thii_Cii and Facebook to be notified on other interesting content when it is posted. Please also share this content with friends who may be interested.
Artwork by @anon_unique #africandigitalart